Toptube Video Search EngineTitle:ZATHU BAND - CHINZATHU ICHICHI
Duration:08:00
Viewed:22,204
Published:11-09-2018
Source:Youtube

Yafika! Video yatsopano ya chinyamata a Zathu Band, yotchedwa ‘chinzathu Ichichi’. Vidiyoyi ikutionetsa momwe makolo angatengele mbali pa moyo wa achinyamata pothandiza kuti anyamata ndi atsikana azigwilila ntchito limodzi, komanso kuthandizana pa zochitika zosiyanasiyana monga zakusukulu komanso zina zambili zomwe zingawathandize kusintha miyoyo yawo. Muona momwe Agogo anathandizila Bambo a JP kumvetsa kuti Mphatso ndI JP amangogwilila ntchito limodzi ndipo panalibe chilichonse pakati pawo. Gogo awathandiza kumvetsa kuti kulola anyamata ndi atsikana kuti agwile ntchito limodzi kungathandize kuti achinyamata akwaniritse komanso kuchita zinthu zazikulu mu moyo komanso dela lawo.SHARE TO YOUR FRIENDS


Download Server 1


DOWNLOAD MP4

Download Server 2


DOWNLOAD MP4

Alternative Download :