Toptube Video Search Engine



Title:Phyzix - CHIKONDI ft. Macia (Official Video) 2022
Duration:03:20
Viewed:217,801
Published:31-01-2022
Source:Youtube

Phyzix, It's Only Entertainment (IOE) Artist/CEO delivers his brand new song 'CHIKONDI' ft. Macia. © 2022 It's Only Entertainment (IOE) Follow Phyzix on Social Media: Facebook: https://www.facebook.com/PhyzixMw/ Twitter: https://twitter.com/PhyzixMw Instagram: https://www.instagram.com/phyzixmw/ Tik Tok: https://www.tiktok.com/@phyzixmw Website: http://www.audiomack.com/artist/phyzix A film by Twice P Director & Editor: Twice P *Chikondi Lyrics by Phyzix & Macia* *(Intro: Phyzix & Macia)* M'bobo dem/ Ayayayaya Phyzix/ Very Good, Very Good Ndimangomvera ma romours Macia/ Ati love is sweet Yeah/ Very Good, Very Good *(Verse 1: Phyzix)* Zimakhala bwino kumakhala 2-2/ umumu ndi momwe tinalengedwela anthu Ndinaipeza nthiti yanga ndine thunthu/ umandikwanira real love is what am into Baby girl Chikondi osabisa/ ndimakunyadila daily kumakukissa/ mtswaaah Osamachoka ndimakumisa/ umandidalitsa When I think of an Angel you the picture/ umandibweletsera mtendere wodabwitsa/ Wanna make sure kuti nthawi ndakupatsa/ olo anthu atanena kuti ndinapusa *(Pre-Chorus: Macia)* Ndimangomva ma romours Ati love is sweet Ndimagwidwa ndi nthumazi yeeeee mwina nkudzathera misonzi *(Chorus: Macia)* Ngati ndalama zikhale Kaya kutchuka kukhale Kukongora kukhale U handsome ukhaleeee Nane ndimafuna chikondi Nane ndimafuna kukondedwa Nane ndimasowa chikondi Nane ndimafuna kukondedwa Oyayaya *(Verse 2: Phyzix)* Let's make everyday Valentine's Day/ tizikondana and not care what people say/ zaka kumapita koma same way/ baby girl you my sunshine let's make hay As your man I promise to love you/ to always be gentle popanda za ganyavu/ I know many guys wanna cuff you/ tiye tizivaya padeni ngati ndi curfew Dancing to the rhythm of a love song/amene akuti tidzasiyanawo they dead wrong The smiles the frowns/ the ups and the downs/ Chikondi sichophweka we just gotta be strong *(Pre-Chorus: Macia)* Ndimangomva ma romours Ati love is sweet Ndimagwidwa ndi nthumazi yeeeee mwina nkudzathera misonzi *(Chorus: Macia)* Ngati ndalama zikhale Kaya kutchuka kukhale Kukongora kukhale U handsome ukhaleeee Nane ndimafuna chikondi Nane ndimafuna kukondedwa Nane ndimasowa chikondi Nane ndimafuna kukondedwa Oyayaya *(Bridge: Macia)* Put aside your pride iwe mwamuna wanga mkazi wanga Kuzitukumula kuononga zinthu mama ayaaa Iyaaaaaa yeeeeeheeeee *(Chorus: Macia)* Ngati ndalama zikhale Kaya kutchuka kukhale Kukongora kukhale U handsome ukhaleeee Nane ndimafuna chikondi Nane ndimafuna kukondedwa Nane ndimasowa chikondi Nane ndimafuna kukondedwa Oyayaya



SHARE TO YOUR FRIENDS


Download Server 1


DOWNLOAD MP4

Download Server 2


DOWNLOAD MP4

Alternative Download :