Toptube Video Search EngineTitle:Theresa Phondo & Kelvin Sings - Assurance (Visualizer)
Duration:03:13
Viewed:127,605
Published:03-05-2022
Source:Youtube

Zaka zambiri zatha Iwe ine tikucheza Mphekesela zinkamveka kuti ife ndi chibwenzi Koma ife tinkakana Timvekere sizingatheke Iwe ndi ine sitilola Lero ndatopa ndi mafunso Omadzifunsa ndekha Ine ndalema ndi mafunso Ondifusanso ena Chifukwa chomwe ndimadziwa Nchoti ndimakukonda Chimodzi chomwe n’funa n’dziwe Ndimve pakamwa pako Ngati umandikondadi ine Umandifunadi ine Ndimafuna ndidziwe Ndidziwe ndidziwe Ndimafuna ndidziwe Ndidziwe ndidziwe Nthawi nde ikupita Nkhawa nde zikubwerabe (bwerabe) Chovuta kodi nchani Kunena m’mene umamvera yeah I need some assurance Munthune ndikukula yeah Nde tangonena Tipange mapulani Kuti zinthu zikhala bwanji Poti ndatopa ndimafunso Omadzifunsa ndekha Ine ndalema ndimafunso Ondifusanso ena Ooh chifukwa chomwe ndimadziwa Iwe ndiamene ndimakonda Chimodzi chomwe n’funa n’dziwe Ndimve pakamwa pako Kodi umandikondadi iwe Oooh umandifunadi iwe Ndimafuna ndidziwe Ndidziwe ndidziwe Ndimafuna ndidziwe Ndidziwe ndidziwe Ooohhh umandikondadi iwe Umandikondadi iwe Ndimafuna ndidziwe Ndidziwe ndidziwe Ndimafuna ndidziwe Ndidziwe ndidziwe Ndidziwe ndidziwe ndidziwe Patseko assurance Ndimafuna ndidziwe ndidziwe ndidziwe Munthune ndikukula Ndidziwe ndidziwe ndidziwe Patseko assurance, munthune ndikukula Ndimafuna ndidziwe ndidziwe ndidziwe Patseko assurance, munthune ndikukulaSHARE TO YOUR FRIENDS


Download Server 1


DOWNLOAD MP4

Download Server 2


DOWNLOAD MP4

Alternative Download :