Toptube Video Search EngineTitle:Phyzix - WIFE MATERIAL ft. Pon G (Official Video) 2021
Duration:03:36
Viewed:628,761
Published:30-08-2021
Source:Youtube

Phyzix, It's Only Entertainment (IOE) Artist/CEO delivers his brand new song 'WIFE MATERIAL' ft. Pon G. In association with WWE Snacks, Kelfoods, Ryalls Hotel and The Bistro. © 2021 It's Only Entertainment (IOE) Follow Phyzix on Social Media: Facebook: https://www.facebook.com/PhyzixMw/ Twitter: https://twitter.com/PhyzixMw Instagram: https://www.instagram.com/phyzixmw/ Tik Tok: @phyzixmw Website: http://www.audiomack.com/artist/phyzix A film by It's Only Entertainment (IOE) Director: Skript Editor: Skript Cinematography: SeanyFilms Photographer: Raz Mirambo Stylist: Chip Nigga Colorist: Skript & Seany ARM: Eric Chan Production Manager: King George Damson Logistics Manager: Macmilly Transport Manager: Evident Location Manager: Phyzix Audio Producer: Pon G Music: Phyzix ft. Pon G Creative Directors: Skript & Seany *Wife Material Lyrics by Phyzix & Pon G* *(INTRO: Phyzix)* Kukakhala kunjaku kwacha bho... yeah/ yeah Kukakhala kunjaku kwacha bho/ zachita kudzadzamo bobobo/ Wifey material/ terial/ terial/ Wifey ma ti ti ti ti *(VERSE 1: Phyzix)* Ndinapeza chibhebhi anthu adziwe/ sindimachibisa sichapadziwe/ yemwe zikumuwawa adhiwe/ koma ichichi ndi changa chi Lindiwe/ sichingazakupatse mphindi iwe chimakhala chili ndi ine uzimva iwe/ vuto lake iweyo kuzimva iwe umangogwira akazi openga ma byzwe/ Za ife ndi zokoma zothila curry/ sitimvetsana kuwawa tsabola wa kale/ Uyuyu ndi wanga si temporary/ ndikanena kuti ndimugaya si mphale/ kutentha ngati Nali samalani abale/ akusungila sugar wonyambititsa mbale/ Mkazi uyu ngoiwalitsa abale/ amakomedwetsa ngati anthu a Ndale/ Very Good Very Good *(HOOK: Pon G & Phyzix)* Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho Mumachita kukhala ngati a M'video Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo Ndinu wifey material terial terial Wifey ma ti ti ti ti Wifey material terial terial Wifey ti ti ti ti *(VERSE 2: Phyzix)* Ichi ndi chi ndiwo koma si mpiru/ sindinachite kuchiba koma ndi chi dhilu/ ichi ndi chibhebhi chodzadza feel/ dzina lake ndinaliyika kale pa will/ chimandikumbutsa Maggie Mwaupighu/ mahope anga a ku Primary ku Mphungu/ tili mafana oyankhula chizungu/ she had a chocolate skin ndimamufila khungu Chibhebhi changachi chandipatsa khungu/ ndikayenda m'townimu sindiona buthu/ Ndadwala Chikondi 10 pa 10/ chachita kundifika pe mpeni/ Ndavomera Mami ndi malizeni/ sindipempha kuti Ambuye ndichilitseni Izi si za gulu si za m'memo/ Ineyo ndili momo m'menemo/ Very Good Very Good *(HOOK: Pon G & Phyzix)* Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho Mumachita kukhala ngati a M'video Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo Ndinu wifey material terial terial Wifey ma ti ti ti ti Wifey material terial terial Wifey ti ti ti ti *(BRIDGE: Pon G & Phyzix)* Gal you di wife material/ I just wanna make you my wife ooh Gal you di one in a million/ this feeling for you I can't deny ooh Iwe ndiwe Mkazi wooneka bho/ wooneka bho/ wooneka bho Iwe ndiwe chi Mkazi chooneka/ chooneka bho/ chooneka bho Iwe ndi Mkazi wofitha bho/ wofitha bho/ wofitha bho Iwe ndi chi Mkazi chofitha bho/ chofitha bho/ chofitha bho *(HOOK: Pon G & Phyzix)* Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho Mumachita kukhala ngati a M'video Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo Ndinu wifey material terial terial Wifey ma ti ti ti ti Wifey material terial terial Wifey ti ti ti tiSHARE TO YOUR FRIENDS


Download Server 1


DOWNLOAD MP4

Download Server 2


DOWNLOAD MP4

Alternative Download :