Toptube Video Search EngineTitle:Lulu and mathumela band - Udzindimvera (Official Music Video)
Duration:03:29
Viewed:448,267
Published:21-04-2023
Source:Youtube

Download Udzindimvera SongπŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡ https://lulu.fanlink.to/StreamUdzindimvera Directed by Chipie Khonje Produced By @mrgravoubeats Mixed and mastered By @mrgravoubeats Management: Mathumela Lulu And Mathumela Band Booking Info: lawrencekhwisamathumela@gmail.com +(265) 99 92 38 947 Catch Up With Lulu And Mathumela Band On: Instagram:https://www.instagram.com/lulu_and_mathumela_band/ Facebook:https://www.facebook.com/lulumathumela?mibextid=ZbWKwL Tiktok:https://www.tiktok.com/@lulumathumelamusic Lyrics πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡ Chorus 1 Udzindimvera udzindimvera pena Udzindimvera udzindimvera baby Udzindimvera udzindimvera pena Udzindimvera udzindimvera baby Verse 1 Palibe muthu amadziwa zonse Zayekha anavika nsima madzi Kuyenda awiri simatha Zodziwa iwe nane singadziwe Kulipo kumafa ndiludzu Kulipo kumanka kutali Kumakafufuza zeru katali Okondeka wanga ndifunse Ndidalile okondeka wanga Ndiyang'ane okendeka wanga Ndidalile okondeka wanga Nditha kukhala opanda Ndalama Koma undidali okondeka wanga Undiyang'ane okondeka wanga Chorus 2 Udzindimvera udzindimvera pena Udzindimvera udzindimvera baby Udzindimvera udzindmivera pena Udzindimvera udzindimvera baby Ngati nkutukuka tidzatukuka tonse Ku shayina ku shayina tonse Udzindimvera udzindimvera baby Dzatuka dzatuka tonse Ku shayina ku shayina tonse Udzindimvera udzindimvera baby Verse 2 Usadzadziwe ntapita kale Usazadzadziwe ine atanditenga Mwendo wanga unali madzi Nanga bwanji ndimafa ndi ludzu Pena ndimavetsa kukula kwako Tasiyana ndife a chimodzi Koma ukadziyi lemekeza ndalama Udzandisiya pa dzuwa Ndidalile okondeka wanga Ndiyang'ane okendeka wanga Ndidalile okondeka wanga Nditha kukhala opanda Ndalama Koma undidali okondeka wanga Undiyang'ane okondeka wanga Chorus 3 Udzindimvera udzindimvera pena Udzindimvera udzindimvera baby Udzindimvera udzindmivera pena Udzindimvera udzindimvera baby Ngati nkutukuka tidzatukuka tonse Ku shayina ku shayina tonse Udzindimvera udzindimvera baby Dzatuka dzatuka tonse Ku shayina ku shayina tonse Udzindimvera udzindimvera baby Β© 2023 Mathumela #luluandmathumelaband #udzimdivera #musicSHARE TO YOUR FRIENDS


Download Server 1


DOWNLOAD MP4

Download Server 2


DOWNLOAD MP4

Alternative Download :