Toptube Video Search EngineTitle:Zathu Band | Panga Zako
Duration:06:10
Viewed:32,907
Published:30-10-2017
Source:Youtube

Nyimbo yachitatu ya achinyamata aja a Zathu Band yatuluka! Nyimboyi ikufotokoza za moyo wa achinyamata asanu ndi mā€™modzi amu Zathu Band komanso Gogo pamene akuthandizana pa zophinja zosiyanasiyana. Mu video imeneyi Chikondi akuvutikabe ndi Aunt Nelly omwe samaona phindu lililonse mu zochitika za achinyamata monga kuimba, kuvina komanso kukhala omasuka ndi moyo wawo. Kodi Chikondi akwanitsa kuwafotokozela Aunt Nelly momveka bwino kuti apite kukaimba ndi achinyamata anzake amu Band? Nkhaniyi ikupitilira bwino mu Season 2 ya Zathu Pa Wailesi.SHARE TO YOUR FRIENDS


Download Server 1


DOWNLOAD MP4

Download Server 2


DOWNLOAD MP4

Alternative Download :